Mawu a M'munsi b Pa nthawi imene anabatizidwa komanso kudzozedwa ndi mzimu woyera, zikuoneka kuti Yesu anakumbukira mmene analili poyamba asanabwere padzikoli.—Mat. 3:16.