Mawu a M'munsi
a MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Chithunzi choyerekezera chosonyeza pamene abale athu a mādziko lomwe linkatchedwa Soviet Union, analandira kalata yooneka ngati yochokera kulikulu lathu koma inali yochokera kwa adani. Masiku ano adani athu angagwiritse ntchito intaneti pofalitsa nkhani zabodza zokhudza gulu la Yehova.