Mawu a M'munsi
a Pa Yesaya 60:1, Baibulo la Dziko Latsopano limagwiritsa ntchito mawu akuti “mkazi” osati “Ziyoni” kapena “Yerusalemu,” chifukwa mawu a Chiheberi omwe anawamasulira kuti “imirira” komanso “onetsa kuwala,” amasonyeza kuti amene akuuzidwayo ndi wamkazi, ngatinso mmene zilili ndi mawu akuti “iwe.”