Mawu a M'munsi
b Mwachitsanzo, nkhani ina m’magazini ina yokhudza banja inati: “Anthu ena anapanga kafukufuku maulendo atatu ndipo anapeza kuti anthu ambiri amene akhala pa banja nthawi yaitali (zaka 25 mpaka 50 kapena zoposa) ndi amene ali m’chipembedzo chimodzi ndipo amakhulupirira zofanana.”—Marriage & Family Review, Voliyumu 38, magazini yoyamba, tsamba 88 (2005).