Mawu a M'munsi
b Dzina lachidule la Mulungu lakuti “Ya” lomwe lilinso m’mawu akuti “Aleluya,” limapezeka nthawi pafupifupi 50 m’Baibulo. Mawu akuti “Aleluya” amatanthauza kuti “Tamandani Ya.”—Chivumbulutso 19:1; Buku Lopatulika Ndilo Mawu a Mulungu.