August Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya August 2017 Zitsanzo za Ulaliki August 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 28-31 Yehova Anapereka Cholowa kwa Anthu Omwe Sankamulambira MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo—Kudzichepetsa August 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 32-34 Udindo Waukulu wa Mlonda MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo—Kulimba Mtima August 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 35-38 Gogi wa ku Magogi Awonongedwa Posachedwapa MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo—Chikhulupiriro August 28–September 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 39-41 Mmene Masomphenya a Ezekieli Onena za Kachisi Akutikhudzira MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Ndingadzachitenso Liti Upainiya Wothandiza?