June Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya June 2018 Zimene Tinganene June 4-10 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIKO 15-16 Yesu Anakwaniritsa Maulosi MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzitsatira Mapazi a Khristu Mosamala Kwambiri June 11-17 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 1 Muzitsanzira Mariya Pokhala Odzichepetsa June 18-24 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 2-3 Ananu, Kodi Mukuyesetsa Kuti Yehova Akhale Mnzanu Wapamtima? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Makolo, Muzithandiza Ana Anu Kuti Azikonda Kwambiri Yehova June 25–July 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 4-5 Muzitsanzira Yesu Pokana Mayesero MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzisamala Mukamacheza ndi Anzanu pa Intaneti