March Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, March-April 2023 March 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kulambira kwa Pakachisi Kunali kwa Dongosolo MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mmene Tingathandizire Pakachitika Ngozi Zadzidzidzi March 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Malangizo Achikondi a Bambo Opita kwa Mwana Wake March 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mfumu Solomo Inasankha Zinthu Mopanda Nzeru Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2023 March 27–April 2 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU ‘Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse’ MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Uteteze Mtima Wako” April 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mfumukazi Inaona Kuti Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muziwerenga Baibulo Tsiku Lililonse Komanso Muzifunafuna Nzeru April 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzitsatira Malangizo Anzeru MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mmene Tingagwiritsire Ntchito Mavidiyo Onena za Kuphunzira Baibulo April 24-30 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene