Mverani (ll) Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa Zamkatimu Mawu Oyamba CHIGAWO 1 Kodi Mulungu Amalankhula Nafe Motani? CHIGAWO 2 Kodi Mulungu Woona Ndani? CHIGAWO 3 Kodi Moyo Unali Wotani m’Paradaiso? CHIGAWO 4 Kodi Chinachitika N’chiyani Adamu ndi Hava Atamvera Satana? CHIGAWO 5 Chigumula Chisanachitike, Kodi Ndani Anamvera Mulungu Ndipo Ndani Amene Sanamumvere? CHIGAWO 6 Kodi Tikuphunzirapo Chiyani pa Zimene Zinachitika Nthawi ya Chigumula? CHIGAWO 7 Kodi Yesu Anali Ndani? CHIGAWO 8 Kodi Imfa ya Yesu Imakukhudzani Bwanji? CHIGAWO 9 Kodi Paradaiso Adzabwera Liti? CHIGAWO 10 Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani? CHIGAWO 11 Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu? CHIGAWO 12 Kodi Mungatani Kuti Aliyense M’banja Mwanu Azisangalala? CHIGAWO 13 Kodi Tiyenera Kuchita Chiyani Kuti Tikondweretse Mulungu? CHIGAWO 14 Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Ndinu Wokhulupirika kwa Yehova?