Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 1/08 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2008
  • Nkhani Yofanana
  • Zidole Zochita Zisudzo
    Galamukani!—2008
  • Kodi Ndizichita Masewera a Pakompyuta?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Kusewera Magemu a Pazipangizo Zamakono?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
  • Kodi Ndiyenera Kuchita Masewera a Pakompyuta?
    Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
Onani Zambiri
Galamukani!—2008
g 1/08 tsamba 1-2

Zamkatimu

January 2008

Kodi Baibulo Limati Chiyani Pamchitidwe Wochitira Nkhanza Akazi?

Padziko lonse akazi akuchitiridwa nkhanza ndiponso kuponderezedwa. Moti zipembedzo zina zafika poyamba kulekerera mchitidwewu. Kodi Baibulo limati chiyani pankhaniyi?

3 Kuchitira Nkhanza Akazi Ndi Vuto la Padziko Lonse

4 Kodi Mulungu ndi Khristu Amaona Akazi Motani?

11 Kamudzi ka Asodzi Kanasintha N’kukhala Mzinda Waukulu

15 Nyama Zakuthengo Zimasangalala ku Gabon

22 Mlatho Umene Unali Kumangidwa Mobwerezabwereza

24 Kangaude

Analengedwadi Mwaluso

25 Nyanja Yapadera Koma Yakufa

28 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Kukhala Mutu Wabanja Kumatanthauza Chiyani Kwenikweni?

30 Zochitika Padzikoli

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Amalikonda Kuposa Chidole Chilichonse

Zidole Zochita Zisudzo 8

Tiyeni tipitire limodzi ku Salzburg, m’dziko la Austria, kuti tikaone zidole zochita zisudzo.

Kodi Ndizichita Masewera a Pakompyuta? 18

Masewera ambiri a pakompyuta amakhala achiwawa komanso a zachiwerewere. Kodi Mkhristu angasankhe bwanji masewera oyenerera? Nanga kodi ayenera kuwononga nthawi yaitali motani akuchita masewerawa? Kodi pali masewera ena amene angachite?

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

By courtesy of the Salzburg Marionette Theatre

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena