Zamkatimu
TSAMBA MUTU
3 Kodi Zimene Zikuchitikazi Ndi Zomwe Mulungu Ankafuna?
8 1. Kodi Mukudziwa Zotani Zokhudza Mulungu?
18 2. Baibulo Ndi Buku Lochokera Kwa Mulungu
27 3. Kodi Mulungu Analenga Dziko Lapansili Chifukwa Chiyani?
37 4. Kodi Yesu Khristu Ndi Ndani?
47 5. Dipo la Yesu Ndi Mphatso ya Mulungu Yamtengo Wapatali Kuposa Zonse
57 6. Kodi Munthu Akafa Amapita Kuti?
66 7. Anthu Amene Anamwalira Adzakhalanso ndi Moyo
76 8. Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani?
86 9. Kodi Tilidi ‘M’masiku Otsiriza’?
96 10. Mmene Zochita za Angelo Komanso Ziwanda Zimakhudzira Moyo Wathu
106 11. N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Anthu Azivutika?
115 12. Khalani ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo
125 13. Muziona Moyo Ngati Mmene Mulungu Amauonera
134 14. Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Lizisangalala
144 15. Kulambira Kumene Mulungu Amavomereza
154 16. Yesetsani Kuti Muzilambira Mulungu M’njira Yovomerezeka
164 17. Pemphero Lingakuthandizeni Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu
174 18. Ubatizo Umatithandiza Kuti Tikhale pa Ubwenzi ndi Mulungu
184 19. Zimene Mungachite Kuti Mulungu Apitirize Kukukondani
194 Zakumapeto