Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 August tsamba 5
  • Yehova Amakumbukira Kuti Ndife Fumbi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Amakumbukira Kuti Ndife Fumbi
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Amakumbukira Kuti “Ndife Fumbi”
    Nsanja ya Olonda—2011
  • “Lemekeza Yehova, Moyo Wanga”
    Nsanja ya Olonda—1999
  • Kodi Mulungu Amakhululuka Machimo Akuluakulu?
    Galamukani!—2008
  • Mulungu “Wokonzeka Kukhululuka”
    Yandikirani Yehova
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 August tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 102-105

Yehova Amakumbukira Kuti Ndife Fumbi

Munthu watenga fumbi m’manja mwake ndipo akuganizira za kumwamba kokhala nyenyezi, dzuwa komanso chifundo chimene bambo amasonyeza mwana wake

Davide akamafotokoza zokhudza kukoma mtima kwa Yehova, ankagwiritsa ntchito mawu oyerekezera.

  • Kumwamba kokhala nyenyezi

    103:11

    N’zosatheka kudziwa bwinobwino kuti kumwamba n’kotalikirana bwanji ndi dziko lapansi. Mofanana ndi zimenezi n’zovutanso kumvetsa kuti kukoma mtima kwa Yehova kumafika pati

  • Dzuwa

    103:12

    Yehova amaika machimo athu kutali kwambiri ndi ife, ngati mmene kum’mawa kwatalikirana ndi kumadzulo

  • Bambo akusonyeza mwana wake chifundo

    103:13

    Mofanana ndi mmene bambo amachitira chifundo mwana wake amene wavulala, nayenso Yehova amachitira chifundo munthu amene akumva chisoni chifukwa cha machimo ake

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena