Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Kodi Baibulo Lingandithandize Ngati Ndili ndi Maganizo Ofuna Kudzipha?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
      • Zimene Baibulo limanena: “Bwenzi lenileni limakukonda nthawi zonse, ndipo bwenzilo ndi m’bale amene anabadwira kuti akuthandize pakagwa mavuto.”—Miyambo 17:17.

        Mfundo yake: Tonsefe timafuna kuti anthu ena atithandize tikakumana ndi mavuto.

        Ngati simungauze anzanu mmene mukumvera, zimakhala ngati mwanyamula chimwala cholemera ndipo simukufuna kuchitula pansi. Koma mukawafotokozera, zimakhala ngati mwachitula ndipo zinthu zimayamba kukuyenderani bwino.

        Munthu amene akulimbana ndi maganizo ofuna kudzipha akufotokozera mnzake
  • Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yokhala Ndi Anzathu?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
    • Miyambo 17:17: “Bwenzi lenileni limakukonda nthawi zonse, ndipo bwenzilo ndi m’bale amene anabadwira kuti akuthandize pakagwa mavuto.”

      Mfundo yake: Anzathu enieni ndi amene amatithandiza pa nthawi zabwino komanso zovuta..

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena