-
Kodi Nchifukwa Ninji Pali Kutaya Mtima Konseko?Nsanja ya Olonda—1992 | July 1
-
-
Mikhalidwe yovuta yochititsidwa ndi ndale zadziko, chiwawa, mavuto achuma, zonsezo zingachititse kutaya mtima. Ngakhale anthu antchito zapamwamba amaphatikizidwa m’vutoli, pamene akuyesayesa kusunga moyo wawo wokhupuka kwinaku akulimbana ndi mavuto achuma omakulakulabe. Nchotulukapo chotani? ‘Chitsenderezo chiyalutsa wanzeru,’ malinga nkunena kwa Mfumu yakale Solomo!a (Mlaliki 7:7) Ndithudi, kutaya mtima kumapangitsa ochuluka kutenga njira yonkitsa kuti atuluke m’vutolo—kudzipha.
-
-
Kodi Nchifukwa Ninji Pali Kutaya Mtima Konseko?Nsanja ya Olonda—1992 | July 1
-
-
a Malinga nkunena kwa Theological Wordbook of the Old Testament, lokonzedwa ndi Harris, Archer, ndi Waltke, liwu la chinenero choyambirira lotembenuzidwa “kutsendereza” limapereka lingaliro la “kuthodwetsa, kupondereza, ndi kukanikiza okhala ndi malo otsika.”
-