Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsamba 6
  • “Kumbukira Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Kumbukira Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Kumbukirani Mlengi Wanu Wamkulu!
    Nsanja ya Olonda—1999
  • Khalani ndi Moyo Wopindulitsa
    Nsanja ya Olonda—1998
  • Achichepere Amene Amakumbukira Mlengi Wawo
    Nsanja ya Olonda—1996
  • Ana Amene Amakondwereta Mtima wa Yehova
    Nsanja ya Olonda—1987
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 November tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MLALIKI 7-12

“Kumbukira Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”

Muzikumbukira Mlengi Wanu Wamkulu pogwiritsa ntchito mphamvu zanu pomutumikira mudakali achinyamata

Mnyamata waima pambali pa munthu wachikulire yemwe akuyendera ndodo

12:2-7

  • Achinyamata ambiri ndi athanzi komanso amphamvu moti akhoza kugwira ntchito zovuta

  • Achinyamata ayenera kugwiritsa ntchito nthawi komanso mphamvu zawo potumikira Mulungu asanayambe kukumana ndi mavuto obwera chifukwa cha ukalamba

Solomo anagwiritsa ntchito mawu andakatulo pofotokoza mavuto amene okalamba amakumana nawo

12:1, 13

  • Azimayi akusuzumira pawindo

    Vesi 3: “Akazi oyang’ana pawindo azidzaona mdima”

    Kuvutika kuona

  • Azimayi akuimba

    Vesi 4: “Ana onse aakazi azidzaimba nyimbo ndi mawu otsika”

    Kuvutika kumva

  • Zipatso

    Vesi 5: Mawu enieni a vesili amanena za kuphulika kwa chipatso chinachake chimene munthu amadya kuti zakudya ziyambirenso kumukomera

    “Zakudya sizidzakoma”

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena