Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsamba 7
  • Dziko Lapansi Lidzadzaza ndi Anthu Odziwa Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Dziko Lapansi Lidzadzaza ndi Anthu Odziwa Yehova
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • “Mawu a Mulungu Ngamoyo Ndipo Amapereka Mphamvu”
    Nsanja ya Olonda​—1990
  • Chifukwa Chimene Timafunikira Chidziŵitso Cholongosoka
    Nsanja ya Olonda—1989
  • “Tidzaonana M’Paradaiso”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • Kodi Mwasandulika?
    Nsanja ya Olonda—2013
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 December tsamba 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 11-16

Dziko Lapansi Lidzadzaza ndi Anthu Odziwa Yehova

Mwana akusewera ndi nyama zakutchire m’Paradaiso

11:6-9

Mmene ulosiwu unakwaniritsidwira m’nthawi ya Aisiraeli

  • Pamene Aisiraeli ankabwerera kuchoka ku ukapolo ku Babulo ndiponso atafika kudziko lawo, sankafunika kuopa zilombo zakutchire kapena anthu amakhalidwe ngati a zilombo.—Ezara 8:21, 22.

Mmene ulosiwu ukukwaniritsidwira masiku ano

  • Kuphunzira za Yehova kwathandiza anthu ambiri kusintha makhalidwe awo. Anthu amene kale anali ankhanza asintha ndipo amakhala mwamtendere ndi anzawo. Kuphunzira za Mulungu kwathandiza kuti padziko lonse pakhale paradaiso wauzimu.

Mmene ulosiwu udzakwaniritsidwire mtsogolo

  • Dziko lonse lapansi lidzasinthidwa kuti likhale lokongola ndipo anthu azidzakhala motetezeka komanso mwamtendere ngati mmene Mulungu ankafunira poyamba. Palibe nyama iliyonse kapena munthu amene azidzapangitsa kuti anthu azikhala mwamantha.

Paulo anasintha chifukwa chophunzira za Mulungu

  • Poyamba anali Mfarisi ndipo anali ndi makhalidwe ngati a chilombo.—1 Tim. 1:13.

  • Kudziwa mfundo zolondola kunamuthandiza kusintha khalidwe lake.—Akol. 3:8-10.

Mtumwi Paulo anasintha khalidwe lake lopsa mtima n’kukhala munthu wofatsa
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena