Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Kuyesedwa ndi Kusefedwa mu Nthawi Zamakono
    Nsanja ya Olonda—1987
    • Kuyesedwa ndi Kusefedwa mu Nthawi Zamakono

      “Koma ndani adzapirira tsiku la kudza kwake? Ndipo adzaima ndani powoneka iye?​—MALAKI 3:2.

      1. Pamene Yehova anabwera ku kachisi wauzimu mu nthawi zamakono, kodi nchiyani chimene iye anapeza, kudzutsa funso lotani?

      PAMENE “Ambuye Wowona” anafika ku kachisi wauzimu limodzi ndi “mthenga wa chipangano,” wake, mwamsanga pambuyo pa kukhazikitsidwa kwa Ufumu kumwamba mu 1914, kodi nchiyani chimene Yehova anapeza? Anthu ake anafunikira kuyengedwa ndi kuyeretsedwa. Kodi iwo akadzigonjetsera iwo eni ku ichi ndi kupirira kuyeretsedwa kofunikira kulikonse kwa gulu lawo, ntchito yawo, ziphunzitso zawo, ndi khalidwe? Monga mmene Malaki analembera icho: “Koma ndani adzapirira tsiku la kudza kwake? Ndipo adzaima ndani powoneka iye?”​—Malaki 3:1, 2.

  • Kuyesedwa ndi Kusefedwa mu Nthawi Zamakono
    Nsanja ya Olonda—1987
    • 3. Pofika mu ngululu ya 1918, kodi ndi uti womwe unali mkhalidwe wa mboni za Mulungu?

      3 Pamene Yehova anapita ndi “mthenga wake wa chipangano” ku kachisi wauzimu, iye anapeza otsalira ali osowa kuyengedwa ndi kuyeretsedwa. Mwachitsanzo, Nsanja ya Olonda inalimbikitsa awerengi ake kuika pambali May 30, 1918, monga tsiku la mapemphero kaamba ka chipambano champhamvu za demokratiki, monga mmene chinafunsidwira ndi U. S. congress ndi Prezidenti Wilson. Ichi chinafikira kukuphwanya kwa uchete wa Chikristu.​—Yohane 17:14, 16.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena