Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsamba 3
  • “Mboni Ziwiri” Zinaphedwa Koma Zinakhalanso ndi Moyo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Mboni Ziwiri” Zinaphedwa Koma Zinakhalanso ndi Moyo
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda—2014
  • “Mafupa Ouma” Komanso ‘Mboni Ziwiri’—Kodi Zikugwirizana Bwanji?
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Mboni Ziwiri Zinaukitsidwa
    Mapeto Osangalatsa a Masomphenya a M’buku la Chivumbulutso
  • Masiku aulosi a Danieli ndi Chikhulupiriro Chathu
    Nsanja ya Olonda—1993
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 December tsamba 3
‘Mboni ziwiri’ zotchulidwa m’buku la Chivumbulutso zaimirira patsogolo pa zoikapo nyale komanso mitengo ya maolivi

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 10-12

“Mboni Ziwiri” Zinaphedwa Koma Zinakhalanso ndi Moyo

11:3-11

  • “Mboni ziwiri”: Gulu laling’ono la abale odzozedwa omwe ankatsogolera pamene Ufumu wa Mulungu unakhazikitsidwa mu 1914

  • Zinaphedwa: Zitalalikira kwa zaka zitatu ndi hafu “zitavala ziguduli,” tinganene kuti mbonizi “zinaphedwa” pamene zinaikidwa m’ndende n’kusiya kugwira ntchito yawo

  • Zinakhalanso ndi moyo: Masiku atatu ndi hafu ophiphiritsawa atatha, mbonizi zinakhalanso ndi moyo pamene zinatuluka m’ndende n’kukapitiriza kutsogolera ntchito yolalikira

Lemba la Chivumbulutso 11:1, 2 limagwirizanitsa zochitika zimenezi ndi ntchito yoyendera komanso kuyeretsa kachisi wauzimu yomwe imafotokozedwa pa Malaki 3:1-3. Tchati chosonyeza ulosi ndi nthawi chikusonyeza: kuyeretsa kachisi komwe kunayamba chakumapeto kwa 1914 mpaka kumayambiriro kwa 1919; zaka zitatu ndi hafu kapena masiku 1,260 kuchokera kumapeto kwa 1914 kudzafika kumayambiriro kwa 1918; masiku atatu ndi hafu omwe ndi kuchokera kumayambiriro kwa 1918 kudzafika kumayambiriro kwa 1919.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena