Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Kodi Muyenera Kukhoma Misonkho?
    Galamukani!—2003 | December 8
    • Taganizirani zimene Yesu analangiza ophunzira ake. Iye ankadziŵa kuti Ayuda anzake ankadana kwambiri ndi misonkho imene Aroma anakhazikitsa. Ngakhale zinali choncho, Yesu anawalimbikitsa kuti: “Perekani zake za Kaisara kwa Kaisara, ndi zake za Mulungu kwa Mulungu.” (Marko 12:17) N’zochititsa chidwi kuti Yesu analimbikitsa kupereka msonkho ku boma limene linali litatsala pang’ono kumupha.

  • Kodi Muyenera Kukhoma Misonkho?
    Galamukani!—2003 | December 8
    • a Langizo la Yesu lopereka “kwa Kaisara zake za Kaisara” silinangonena za msonkho wokha ayi. (Mateyu 22:21) Buku lakuti Critical and Exegetical Hand-Book to the Gospel of Matthew, lomwe analemba ndi Heinrich Meyer, limafotokoza kuti: “Mawu akuti [zake za Kaisara] . . . sakutanthauza misonkho ya boma yokha ayi, koma chilichonse chimene Kaisara anayenera kupatsidwa chifukwa chakuti anali wolamulira.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena