Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp20 No. 2 tsamba 3
  • “Ufumu Wanu Udze”​​​—Pemphero Limene Anthu Ambiri Amalikonda

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Ufumu Wanu Udze”​​​—Pemphero Limene Anthu Ambiri Amalikonda
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
    Nsanja ya Olonda—2014
  • N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudziwa za Ufumu wa Mulungu?
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
  • Ufumu wa Mulungu
    Galamukani!—2013
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
wp20 No. 2 tsamba 3
Anthu amitundu komanso misinkhu yosiyanasiyana akupemphera.

“Ufumu Wanu Udze”​—Pemphero Limene Anthu Ambiri Amalikonda

Kodi nthawi ina munapempherapo kuti Ufumu wa Mulungu ubwere? Kwa zaka zambiri, anthu akhala akunena mawu oti “Ufumu wanu udze” akamapemphera. Anthu amakonda kutchula mawu amenewa chifukwa choti Yesu anauza otsatira ake kuti azipempherera Ufumu wa Mulungu.

Poyamba, otsatira a Yesu sanamvetse zinthu zonse zomwe Yesu ankaphunzitsa zokhudza Ufumuwu. Pa nthawi ina iwo anamufunsa kuti: “Ambuye, kodi mubwezeretsa ufumu kwa Isiraeli pa nthawi ino?” N’kutheka kuti anadabwa kwambiri chifukwa choti Yesu sanawauze nthawi yeniyeni yomwe Ufumuwo udzabwere. (Machitidwe 1:6, 7) Koma kodi zimenezi zikutanthauza kuti sitingadziwe kuti Ufumu wa Mulungu n’chiyani, ndiponso kuti udzabwera liti? Ayi.

Nsanja ya Olondayi ikuthandizani kupeza mayankho a mafunso otsatirawa:

  • N’chifukwa chiyani tikufunikira Ufumu wa Mulungu?

  • Kodi Mfumu ya Ufumu wa Mulungu ndi ndani?

  • Kodi Ufumu wa Mulungu udzayamba liti kulamulira dzikoli?

  • Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita zotani?

  • N’chifukwa chiyani tiyenera kukhala kumbali ya Ufumu wa Mulungu panopa?

  • Kodi Ufumu wa Mulungu n’chiyani?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena