Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Kodi Tizitchula Zinthu Ziti Tikamapemphera kwa Mulungu?
    Galamukani!—2012 | February
    • Yesu ananena kuti: “Koma inu muzipemphera motere: ‘Atate wathu wakumwamba, dzina lanu liyeretsedwe. Ufumu wanu ubwere. Chifuniro chanu chichitike, monga kumwamba, chimodzimodzinso pansi pano. Mutipatse ife lero chakudya chathu chalero. Mutikhululukire zolakwa zathu monga mmene ifenso takhululukira amene atilakwira. Musatilowetse m’mayesero, koma mutilanditse kwa woipayo.’”—Mateyu 6:9-13.

  • Kodi Tizitchula Zinthu Ziti Tikamapemphera kwa Mulungu?
    Galamukani!—2012 | February
    • “Musatilowetse m’mayesero, koma mutilanditse kwa woipayo.” “Woipa” amene akutchulidwa palembali ndi Satana Mdyerekezi, yemwe amadziwikanso kuti “Woyesayo.” (Mateyu 4:3) Chifukwa cha kupanda kwathu ungwiro, timafunika kuti Mulungu atithandize kulimbana ndi Satana komanso anthu amene amachita zofuna zake.—Maliko 14:38.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena