-
Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Miliri?Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
-
-
Kodi Baibulo linaneneratu za miliri?
Baibulo silitchula mayina a miliri monga COVID-19, Edzi, TB, malungo kapena chimfine cha ku Spain. Koma linaneneratu kuti “kudzakhala miliri” ndi “mliri wakupha.” (Luka 21:11; Chivumbulutso 6:8) Miliri imeneyi ndi mbali ya chizindikiro cha “masiku otsiriza” omwe amatchedwanso “mapeto a nthawi ino.”—2 Timoteyo 3:1; Mateyu 24:3.
-
-
Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Miliri?Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
-
-
Luka 21:11: “Kudzakhala miliri.”
Tanthauzo lake: Matenda amene akufalikira padziko lonse, ndi mbali ya chizindikiro cha masiku otsiriza.
-