Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 July tsamba 5
  • “Ndinu Ofunika Kwambiri Kuposa Mpheta Zambiri”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Ndinu Ofunika Kwambiri Kuposa Mpheta Zambiri”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Amene Amaona Kuti Ndife Ofunika Kwambiri
    Nsanja ya Olonda—2008
  • Yehova Amawerenga ‘Tsitsi Lonse la M’mutu Mwanu’
    Nsanja ya Olonda—2005
  • Ndinu Wofunika Kwambiri kwa Mulungu!
    Galamukani!—1999
  • Tisamaiwale Kupempherera Akhristu Amene Akuzunzidwa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 July tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 12-13

“Ndinu Ofunika Kwambiri Kuposa Mpheta Zambiri”

12:6, 7

Mpheta ziwiri

Kodi n’chiyani chomwe chinachititsa Yesu kunena mawu a pa Luka 12:6, 7? Mu vesi 4, Yesu anauza ophunzira ake kuti asamaope anthu omwe amawatsutsa kapena amene amafuna kuwapha. Yesu ankafuna kuti ophunzira ake akhale okonzeka kuti asadzavutike akadzayamba kutsutsidwa. Iye anawatsimikizira kuti Yehova amaona kuti atumiki ake ndi amtengo wapatali ndipo sangalole kuti chikhulupiriro chawo chiwonongeke.

Kodi tingatengere bwanji chitsanzo cha Yehova pa nkhani yoganizira anthu omwe akuzunzidwa?

Kodi tingapeze kuti nkhani zonena za a Mboni za Yehova omwe ali m’ndende chifukwa cha chikhulupiriro chawo?

Kodi panopo ndi abale ndi alongo angati amene ali m’ndende?

M’bale akupemphera ali m’ndende
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena