Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsamba 7
  • Yesu Anachitira Umboni Choonadi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yesu Anachitira Umboni Choonadi
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Akristu Amalambira Mumzimu ndi M’choonadi
    Nsanja ya Olonda—2002
  • Taphunzitsidwa Kuchitira Umboni Mokwanira
    Nsanja ya Olonda—2005
  • Kodi Nkufuniranji Choonadi?
    Nsanja ya Olonda—1995
  • “Mpaka Kumalekezero a Dziko Lapansi.”
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 October tsamba 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 18-19

Yesu Anachitira Umboni Choonadi

18:36-38a

Yesu anachitira umboni choonadi chokhudza zolinga za Mulungu

  • M’MAWU: Iye ankalalikira mwakhama choonadi chonena za Ufumu wa Mulungu

  • M’ZOCHITA: Zimene anachita pa moyo wake zinasonyeza kuti maulosi a m’Baibulo ndi olondola

Nafenso monga otsatira a Yesu, timachitira umboni choonadi

  • M’MAWU: Ngakhale ena azitinyoza, timalalikira mwakhama uthenga wabwino wonena za Ufumu wa Mulungu womwe Mfumu yake ndi Yesu Khristu

  • M’ZOCHITA: Timasonyeza kuti tili ku mbali ya ulamuliro wa Yesu tikamachita zimene Mulungu amafuna komanso tikamapewa kukhala mbali ya dziko

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi anthu ena amatha kuona bwinobwino kuti chofunika kwambiri pa moyo wanga ndi kuchitira umboni choonadi?’

Alongo akuonetsa vidiyo mayi wina; m’bale akulalikira bambo wina pagalaja; makolo akupanga kulambira kwa pabanja ndi ana awo; mlongo akulalikira mnzake wa kuntchito
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena