-
Paulo Achitira Umboni Molimba Mtima Pamaso pa ZindunaNsanja ya Olonda—1998 | September 1
-
-
Choyamba, Paulo anauza Agripa kuti kale ankazunza Akristu. ‘Ndinawakakamiza anene zamwano,’ iye anatero. “Ndinawalondalonda ndi kuwatsata ngakhale kufikira ku midzi yakunja.” Kenaka Paulo ananenanso za mmene anaonera masomphenya ochititsa chidwi pamene Yesu woukitsidwayo anamfunsa kuti: “Undilondalonderanji ine? Nkukuvuta kutsalima pachothwikira.”a—Machitidwe 26:4-14.
-
-
Paulo Achitira Umboni Molimba Mtima Pamaso pa ZindunaNsanja ya Olonda—1998 | September 1
-
-
a Mawu akuti “kutsalima pachothwikira” akufotokoza za mmene ng’ombe yamagoli imadzivulazira ngati itsalimira patsatsa loŵaŵa. Mofananamo, pamene anali kuzunza Akristu, Saulo akanangodzipweteka, popeza kuti anali kumenyana ndi anthu omwe anali kuchirikizidwa ndi Mulungu.
-