-
Ntchito ya Alembi Akale Yokopera Mawu a MulunguNsanja ya Olonda—2007 | March 15
-
-
Kale Alembi Analiko ku Isiraeli
Mose anakulira m’banja la Farao. (Eksodo 2:10; Machitidwe 7:21, 22) Akatswiri a mbiri ya Iguputo wakale amati zimene Mose anaphunzira zingaphatikizepo kuwerenga ndi kulemba bwino kalembedwe ka Aiguputo komanso zina ndi zina za ntchito yaulembi. M’buku lake, pulofesa James K. Hoffmeier anati: “M’pake kukhulupirira zimene Baibulo limanena kuti Mose ankatha kulemba zochitika, maulendo, ndi zinthu zina zokhudzana ndi ntchito yaulembi.”b—Israel in Egypt.
-
-
Ntchito ya Alembi Akale Yokopera Mawu a MulunguNsanja ya Olonda—2007 | March 15
-
-
b Umboni wakuti Mose analemba nkhani zamalamulo umapezeka pa Eksodo 24:4, 7; 34:27, 28 ndi pa Deuteronomo 31:24-26. Nyimbo imene analemba imatchulidwa pa Deuteronomo 31:22, ndipo nkhani yonena za ulendo wawo m’chipululu imatchulidwa pa Numeri 33:2.
-