Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ‘Kuzindikira Zimene Ife Tiri’—Panthawi ya Chikumbutso
    Nsanja ya Olonda—1990 | February 15
    • 3 “Ambuye Yesu usiku uja anaperekedwa, anatenga mkate; ndipo mmene adayamika, ananyema, naati, Ichi ndithupi langa la kwa inu; chitani ichi chikhale chikumbukiro changa. Koteronso chikho, chitatha chakudya, ndi kuti, Chikho ichi ndipangano latsopano m’mwazi wanga; chitani ichi, nthaŵi zonse mukamwa, chikhale chikumbukiro changa. Pakuti nthaŵi zonse mukadya mkate uwu ndi kumwera chikho, mulalikira imfa ya Ambuye kufikira akadza Iye.”​—1 Akorinto 11:23-26.a

    • a “Pausiku umene Iye anaperekedwa Ambuye Yesu anatenga mkate; atayamika, anaunyema nati: ‘Iri ndithupi langa kaamba ka inu; chitani ichi monga chondikumbukira.’ Mofananamo Iye anatenga chikho pamene chakudya chamadzulo chinali chitatha, ndipo adaati: ‘Chikho ichi ndicho pangano latsopano, lotsimikiziridwa ndi mwazi wanga; nthaŵi iriyonse imene muchimwa, mutero kundikumbukira.’”​—An Expanded Paraphrase of the Epistles of Paul, lolembedwa ndi F. F. Bruce.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena