Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera M’dzina la Yesu?
    Nsanja ya Olonda—2008 | February 1
    • Pofuna kuti timvetse kukula kwa udindo wa Yesu, Baibulo limagwiritsa ntchito mawu osiyanasiyana omulemekezera. Zimenezi zimatithandiza kuzindikira madalitso ambiri amene timapeza chifukwa cha zimene Yesu anatichitira, akutichitira ndiponso adzatichitire. (Onani bokosi la mutu wakuti “Udindo Wofunika wa Yesu”.) Ndithudi, Yesu anapatsidwa “dzina loposa lina lililonse.”a Ulamuliro wonse kumwamba ndi padziko lapansi unapatsidwa kwa iye.​—Afilipi 2:9; Mateyo 28:18.

  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera M’dzina la Yesu?
    Nsanja ya Olonda—2008 | February 1
    • a Malinga ndi buku lina (Vine’s Expository Dictionary of New Testament Words), mawu achigiriki amene anawamasulira kuti “dzina” angatanthauze “zimene dzinalo limaimira, udindo, makhalidwe apadera, ulamuliro, mphamvu, [ndi] ulemerero.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena