Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Kudzichinjiriza Kodi Mkristu Ayenera Kufika Pati?
    Galamukani!—1991 | July 8
    • George Napper akupereka uphungu uwu: “Mwinamwake njira yabwino koposa yodzitetezerera inumwini ndiyo kuika pachiswe katundu wanu mmalo mwa moyo wanu. Mbala zambiri ndi othyola amafuna kuba, osati kupha.” M’mikhalidwe pamene munthu wangowopsezedwa kapena pamene ndalama zake zikufunidwa, lamulo labwino nlakuti: ‘Kapolo wa Ambuye sayenera kuchita ndewu.’—2 Timoteo 2:24.a

  • Kudzichinjiriza Kodi Mkristu Ayenera Kufika Pati?
    Galamukani!—1991 | July 8
    • a Pamene kuli kwakuti mawu apatsogolo ndi pambuyo amasonyeza kuti Paulo panopa anali kusonya ku ndewu zapakamwa, liwu la chinenero choyambirira lomasuliridwa ‘ndewu’ (maʹkhe·sthai) mwachisawawa nlogwirizanitsidwa ndi kumenyana ndi zida kapena ndi manja.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena