Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsamba 7
  • Yesetsani Kuti Mulowe Mumpumulo wa Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yesetsani Kuti Mulowe Mumpumulo wa Mulungu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mpumulo wa Mulungu N’chiyani?
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga
    Nsanja ya Olonda—2001
  • Kodi Mwalowa mu Mpumulo wa Mulungu?
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Kodi Mwaloŵa Mpumulo wa Mulungu?
    Nsanja ya Olonda—1998
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 August tsamba 7
Mwamuna ndi mkazi wake ali m’Paradaiso ndipo akuyang’ana dzuwa lomwe likulowa ndipo anthu ena akudya

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 4-6

Yesetsani Kuti Mulowe Mumpumulo wa Mulungu

4:11

Tikhoza kulowa mumpumulo wa Yehova tikamayesetsa kuchita zinthu mogwirizana ndi cholinga chake chomwe amatiuza kudzera m’gulu lake. Tingadzifunse kuti: ‘Kodi ndimachita zotani ndikapatsidwa uphungu? Kodi ndimatani pakakhala kusintha pa nkhani ya mmene timamvera Malemba?’

Kodi ndi mayesero ati omwe angachititse kuti ndisamvere Yehova?

Abale awiri akuthandiza mlongo pogwiritsa ntchito Malemba; m’bale akuphunzira Baibulo payekha ndipo akuona malemba omwe tikuwamva mosiyana ndi kale
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena