-
Mungatani Kuti Banja Lanu Likhale Losangalala?—Mbali YachiwiriMungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
-
-
4. Muziphunzitsa ana anu mwachikondi
Kuphunzitsa mwana si ntchito yamasewera. Koma kodi Baibulo lingakuthandizeni bwanji? Werengani Yakobo 1:19, 20, kenako mukambirane mafunso awa:
Kodi makolo angasonyeze bwanji chikondi akamalankhula ndi ana awo?
N’chifukwa chiyani makolo akakwiya sayenera kulangiza ana awo pa nthawi imeneyo?a
-
-
Mungatani Kuti Banja Lanu Likhale Losangalala?—Mbali YachiwiriMungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
-
-
a M’Baibulo, mawu akuti “malangizo” amatanthauza kuphunzitsa, kutsogolera komanso kuthandiza munthu kuti asinthe. Koma satanthauza kuzunza kapena kuchitira munthu nkhanza.—Miyambo 4:1.
-