Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Kodi Mulungu Analiuzira Motani Baibulo?
    Nsanja ya Olonda—1997 | June 15
    • Ngati Mulungu mwini sanamvumbulire mlembi zochitika, iye Mulungu anali kudziŵitsa wina kotero kuti zimenezo zikhale mbiri yapakamwa kapena yolembedwa, yomwe mbadwo wina unapatsira wotsatira mpaka italembedwa m’Baibulo. (Onani bokosi patsamba 7.) Mulimonse momwe zinalili, tikhulupirira kuti Yehova ndiye anapereka chidziŵitso chonse chimenecho, ndipo anatsogoza alembi ake ncholinga choti zolemba zawo zisakhale ndi zolakwa, kusinjirira, kapena nthano. Za ulosi, Petro analemba kuti: “Anthu a Mulungu, ogwidwa ndi Mzimu Woyera, analankhula.”b​—2 Petro 1:21.

  • Kodi Mulungu Analiuzira Motani Baibulo?
    Nsanja ya Olonda—1997 | June 15
    • b Mtundu wina wa liwu lachigiriki lotembenuzidwa panopa kuti “ogwidwa,” pheʹro, wagwiritsidwa ntchito pa Machitidwe 27:15, 17 kufotokoza chombo chotengeka ndi mphepo. Choncho mzimu woyera ‘unawongola njira’ ya olemba Baibulo. Unawasonkhezera kusiya chidziŵitso chonyenga ndi kuikamo kokha choona.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena