Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsamba 2
  • Khamu Lalikulu la Anthu Likudalitsidwa ndi Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Khamu Lalikulu la Anthu Likudalitsidwa ndi Yehova
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Khamu Lalikulu Lopereka Utumiki Wopatulika
    Nsanja ya Olonda—1995
  • Khamu Lalikulu Kwambiri
    Mapeto Osangalatsa a Masomphenya a M’buku la Chivumbulutso
  • Khamu Lalikulu Loimirira ku Mpando Wachifumu wa Yehova
    Lambirani Mulungu Woona Yekha
  • “Ndinaona Khamu Lalikulu la Anthu”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 December tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 7-9

Khamu Lalikulu la Anthu Likudalitsidwa ndi Yehova

7:9, 14-17

Khamu lalikulu la anthu lavala mikanjo yoyera ndipo lanyamula nthambi zakanjedza m’manja mwawo.

N’chifukwa chiyani Yehova amadalitsa khamu lalikulu?

  • Ali “pamaso pa mpando wachifumu wa [Yehova],” ndipo amamutumikira ndi mtima wonse posonyeza kuti ali kumbali ya ulamuliro wake

  • Avala “mikanjo yoyera,” zomwe zikusonyeza kuti iwo ndi oyera ndipo Yehova amawaona kuti ndi olungama chifukwa amakhulupirira nsembe ya Khristu

  • Akuchita “utumiki wopatulika usana ndi usiku,” ndipo amachita zimenezi nthawi zonse komanso mwakhama kwambiri

Kodi ndingatani kuti ndikhale nawo m’khamu lalikulu?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena