Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 109
  • Tizikondana Kwambiri Kuchokera Mumtima

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tizikondana Kwambiri Kuchokera Mumtima
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Kulani M’chikondi
    Nsanja ya Olonda—2001
  • Kondani Mulungu Amene Amakukondani
    Nsanja ya Olonda—2006
  • Kodi Tingatani Kuti Tizikondana Kwambiri?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • “Uzikonda Yehova Mulungu Wako”
    Nsanja ya Olonda—2014
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 109

NYIMBO 109

Tizikondana Kwambiri Kuchokera Mumtima

Losindikizidwa

(1 Petulo 1:​22)

  1. 1. Tikakhala ndi chikondi

    Timasangalatsa M’lungu.

    Mulungu ndiye chikondi,

    Ndi zosangalatsa.

    Nafe timakonda anthu,

    Timapezadi anzathu.

    Tizisonyeza chikondi

    Chomwe n’chenicheni.

    Ena akavutika

    Tiziwathandiza mwamsanga.

    Tizikhala anzawo

    Omwe amamvetsetsa.

    Yesu anatisonyeza

    Chikondi cha M’lungu wathu.

    Chimatikhudzadi mtima.

    Tizikonda anzathu

    Kuchokera mumtima.

(Onaninso 1 Pet. 2:​17; 3:8; 4:8; 1 Yoh. 3:​11.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena