Nyimbo 2
Kumvera Mulungu Koposa Anthu
1. Tikondweretsa Mulungu;
Tinasiya dziko.
Anthu oipa atida,
Koma sitileka.
Tifuna kumvera M’lungu
Koposa anthuwo.
Timachita zinthu zonse
Modalira Iye.
2. Za “Kaisara” timpatsa,
Ndi olamulira.
Kwa Yehova mkhalidwewo
Usonya ulemu.
Koma poti tinagudwa
Sitiri a ife,
Tikumbuka malangizo
Kutumikira Ya.
3. Tikatamatu Yehova
Mtendere ndiwathu,
Tisayende muuchi mo
Kape na mundewu.
Timatumikira M’lungu,
Ndi kumpatsa zake,
Mosawopa tiri mboni
Za Ufumu wake.
4. Ntchito yathu imayamba.
Sitidzathupsidwa,
Poti ambiri ngaludzu;
Alaŵetu Mawu.
Ena akadodometsa,
Tidziŵa zochita:
Kumvera Mulungu wathu;
Sadzatisiyatu!