Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Kugonana
    Kukambitsirana za m’Malemba
    • 6:9-11) Mudzawona kuti ena a amene anafikira kukhala Akristu poyamba anali ndi chizoloŵezi cha kugonana kwa aziŵalo zofanana. Koma chifukwa cha kukonda kwawo Mulungu, ndi chithandizo cha mzimu wake, anasintha.’

      Kapena munganene kuti: ‘M’kuyankha funsolo, ndinganene kuti ndawona kuti ochuluka amene amalingalira kuti palibe chochititsa manyazi chimene chiyenera kugwirizanitsidwa ndi njira ya moyo ya kugonana kwa aziŵalo zofanana samakhulupirira kuti Baibulo ndilo Mawu a Mulungu. Tandilolani ndikufunseni mmene mumawonera Baibulo?’ Ngati munthuyo anena kuti amakhulupirira Baibulo, mwinamwake mungawonjezere kuti: ‘Kugonana kwa aziŵalo zofanana sindiko nkhani yatsopano. Baibulo limasonyeza lingaliro losasintha la Mulungu mwa mawu omvekera bwino kwambiri. (Mwinamwake gwiritsirani ntchito chidziŵitso cha patsamba 180, 181.)’ Ngati munthu asonyeza chikaikiro ponena za kukhalako kwa Mulungu kapena ponena za Baibulo, mungakhoze kuwonjezera kuti: ‘Ngati panalibe Mulungu, ife mwachiwonekere sitikanakhala ndi thayo kwa iye ndipo chotero tikanakhala ndi moyo monga momwe tifunira. Chotero funso lenileni nlakuti, Kodi pali Mulungu ndipo kodi kukhalapo kwanga kukuchokera kwa iye [ndiponso, mwinamwake, Kodi Baibulo nlouziridwa ndi Mulungu]’ (Gwiritsirani ntchito mfundo za patsamba 306-313 kapena 52-62.)’

  • Kuipa
    Kukambitsirana za m’Malemba
    • Kuipa

      Tanthauzo: Choipa kwambiri mwa makhalidwe. Kaŵirikaŵiri chimatanthauza chinthu chovulaza, chakupha, kapena cha chisonkhezero chowononga.

      Kodi nchifukwa ninji pali kuipa kochuluka?

      Mulungu sangaimbidwe mlandu. Iye anapatsa anthu chiyambi changwiro, koma anthu asankha kunyalanyaza malamulo a Mulungu ndi kudzisankhira chabwino ndi choipa. (Deut. 32:4, 5; Mlal. 7:29; Gen. 3:5, 6) Mwa kuchita izi, adziloŵetsa m’chisonkhezero cha makamu oipa auzimu.—Aef. 6:11, 12.

      1 Yoh. 5:19: “Dziko lonse lapansi ligona mwa woipayo.”

      Chiv. 12:7-12, NW: “Nkhondo inaulika m’mwamba . . . chinjoka ndi angelo ake chinachita nkhondo koma sichinalakika, ngakhale malo sanapezeka konse kaamba ka iwo

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena