Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 105
  • Zakumwamba Zimalengeza Ulemerero wa Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zakumwamba Zimalengeza Ulemerero wa Mulungu
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Kumwamba Kumalengeza Ulemerero wa Mulungu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Miyamba Imalengeza Ulemelero wa Mulungu
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Zolengedwa Zimasonyeza Ulemerero wa Yehova
    Imbirani Yehova
  • M’patseni Yehova Ulemerero
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 105

Nyimbo 105

Zakumwamba Zimalengeza Ulemerero wa Mulungu

Losindikizidwa

(Salimo 19)

1. Kumwamba kumatamanda Yehova.

Ntchito za manja ’ke Timazionatu.

Nthawi zonse zimamutamanda,

Nyenyezi zimasonyeza Kuti ndi wamphamvu.

2. Malamulo a M’lungu ndi angwiro,

Zikumbutso zake Zimatetezadi.

Zigamulo zake n’zolondola.

Mawu ake n’ngolungama. N’ngokoma kwambiri.

3. Kuopa Mulungu ndi kwamuyaya.

Malamulo ake Aposa golide.

Iwotu amatitsogolera.

Dzina lake loyeralo Tililemekeze.

(Onaninso Sal. 111:9; 145:5; Chiv. 4:11)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena