Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 October tsamba 6
  • ‘Muzikumbukira Kukhalapo kwa Tsiku la Yehova’

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • ‘Muzikumbukira Kukhalapo kwa Tsiku la Yehova’
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • “Khalani Oyera”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Kodi Muli ndi Mtima Wodikira?
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Onjezerani Kudzipereka kwa Mulungu pa Chipiriro Chanu
    Nsanja ya Olonda—2002
  • Kodi Muyenera Kukhala Anthu Otani?
    Utumiki Wathu wa Ufumu—1995
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 October tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 PETULO 1-3

‘Muzikumbukira Kukhalapo kwa Tsiku la Yehova’

3:11, 12

Yehova adzabweretsa chiweruzo pa nthawi imene anakonza. Kodi zochita zathu zimasonyeza kuti takonzekera kubwera kwa tsiku limeneli?

Kodi ‘kukhala anthu akhalidwe loyera ndiponso kuchita ntchito zosonyeza kuti ndinu odzipereka kwa Mulungu’ kumatanthauza chiyani?

  • Kumatanthauza kutsatira mfundo za Yehova pa nkhani ya mmene tiyenera kuonera zinthu zabwino kapena zoipa komanso kusagonja ena akamatsutsa zimene timakhulupirira

  • Kumatanthauza kuyesetsa nthawi zonse kuchita zinthu zokhudza kulambira kwathu, tikakhala kwatokha kapena pagulu

Banja likuganizira mmene moyo wawo unalili pamene ankathera nthawi yawo yambiri akuonera TV komanso kugula zinthu ndipo akuyerekezera mmene moyo wawo ulili panopa pomwe amathera nthawi yambiri akulalikira m’malo opezeka anthu ambiri komanso kuchita kulambira kwa pabanja

Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimadziwa kuti tsiku la Yehova layandikira?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena