Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 January tsamba 3
  • Kodi Mungafotokoze Bwanji Zimene Mumakhulupirira?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungafotokoze Bwanji Zimene Mumakhulupirira?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Dokotala Woona za Mafupa Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake
    Galamukani!—2013
  • Kodi Zinthu Zinachita Kulengedwa?—Gawo 3: N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kukhulupirira Kuti Zinthu Zinachita Kulengedwa?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
  • Kodi Zinthu Zinachita Kulengedwa?​—Gawo 4: Kodi Ndingafotokozere Bwanji Munthu Kuti Zinthu Zinachita Kulengedwa?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
  • Kodi Zinthu Zinachita Kulengedwa?—Gawo 1: N’chifukwa Chiyani Ndimakhulupirira Kuti Kuli Mulungu?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 January tsamba 3
M’bale ali kuntchito ndipo akuwerengera lemba munthu wina pa nthawi yopuma masana.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Mungafotokoze Bwanji Zimene Mumakhulupirira?

Kodi munthu atakufunsani kuti n’chiyani chimakupangitsani kukhulupirira kuti zinthu zinachita kulengedwa, mungamuyankhe bwanji? Kuti muyankhe bwino funsoli, mungafunike kuchita zinthu ziwiri izi: Choyamba, inuyo panokha muyenera kutsimikizira kaye kuti zinthu zinachita kulengedwa. (Aroma 12:1, 2) Ndipo chachiwiri, muyenera kudziwa mmene mungafotokozere zomwe mumakhulupirirazo.​—Miy. 15:28.

ONERANI VIDIYO YAKUTI, DOKOTALA WOONA ZA MAFUPA AKUFOTOKOZA ZA CHIKHULUPIRIRO CHAKE KOMANSO YAKUTI KATSWIRI WOONA ZA ZINTHU ZAMOYO AKUFOTOKOZA ZA CHIKHULUPIRIRO CHAKE, KUTI MUONE ZIFUKWA ZIMENE ZINACHITITSA ANTHU ENA KUYAMBA KUKHULUPIRIRA KUTI ZINTHU ZINACHITA KULENGEDWA. KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Chithunzi cha bondo la munthu.

    N’chifukwa chiyani Irène Hof Laurenceau anayamba kukhulupirira kuti zinthu zinachita kulengedwa?

  • Yaroslav Dovhanych.

    N’chifukwa chiyani Yaroslav Dovhanych anayamba kukhulupirira kuti zinthu zinachita kulengedwa?

  • Munthu wina atakufunsani chifukwa chake mumakhulupirira kuti zinthu zinachita kulengedwa, kodi mungafotokoze bwanji?

  • Kodi gulu linatulutsa zinthu ziti m’chinenero chanu zomwe zingakuthandizeni inuyo komanso anthu ena kudziwa kuti Mulungu ndi amene analenga zinthu zonse?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena