Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 16
  • Dzitetezeni kwa Anthu Ampatuko

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Dzitetezeni kwa Anthu Ampatuko
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woyang’anira Dera wa 2025-2026
  • Kodi Tingatani Kuti Tisiye Kukayikira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2025-202
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 16

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Dzitetezeni kwa Anthu Ampatuko

Satana ndi anthu ake nthawi zambiri amasakaniza choonadi ndi bodza pofuna kufooketsa chikhulupiriro chathu. (2Ak 11:3) Mwachitsanzo, Asuri sanafotokoze mmene nkhani yonse inalili ndipo ananena zinthu zabodza pofuna kufooketsa anthu a Yehova. (2Mb 32:10-15) Ampatuko amachitanso zimenezi masiku ano. Kodi tizitani ndi zimene ampatuko amaphunzitsa? Tiziwaona kuti ndi poizoni. Tisamawerenge nkhani zawo, tisamawayankhe komanso tisamaonere mavidiyo awo. Tizizindikira mwamsanga komanso kukana zinthu zomwe zakonzedwa n’cholinga chakuti zitichititse kukayikira Yehova komanso gulu lake.​—Yuda 3, 4.

Chithunzi cha muvidiyo yakuti “‘Menya Mwamphamvu Nkhondo Yachikhulupiriro.’” M’bale David Splane wa m’Bungwe Lolamulira.

ONERANI MBALI INA YA VIDIYO YAKUTI “MENYA MWAMPHAMVU NKHONDO YACHIKHULUPIRIRO,” KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • N’chifukwa chiyani tiyenera kukhala osamala tikamagwiritsa ntchito intaneti?

  • Kodi tingatsatire bwanji malangizo opezeka pa Aroma 16:17?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena