Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 97
  • Mawu a Mulungu Amatithandiza Kukhala Ndi Moyo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu a Mulungu Amatithandiza Kukhala Ndi Moyo
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Moyo Wopanda Mapeto—Potsiriza!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Moyo Wosatha Ulonjezedwa
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Kodi Munalawako Chakudya Chopatsa Moyo?
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Muzikonda Kwambiri Choonadi Panokha
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 97

NYIMBO 97

Mawu a Mulungu Amatithandiza Kukhala ndi Moyo

Losindikizidwa

(Mateyu 4:4)

  1. 1. Moyo umafunikira

    Mawu a Mulungu

    Kuti atitsogolere

    M’zonse timachita,

    Ndipo timasangalala

    Ndi kudalitsidwa.

    (KOLASI)

    Chakudya chofunikira

    Ndi Mawu a M’lungu.

    Moyo umafunikadi

    Mawu a Mulungu.

  2. 2. M’mawuwo timawerenga

    Za anthu akale

    Omwe anatumikira

    Mokhulupirika.

    Tikawerenga nkhanizi

    Zimalimbikitsa.

    (KOLASI)

    Chakudya chofunikira

    Ndi Mawu a M’lungu.

    Moyo umafunikadi

    Mawu a Mulungu.

  3. 3. Tikamawerenga Mawu

    Tsiku lililonse,

    Tidzathadi kupirira

    Mayesero onse.

    Ndiye tizikumbukira

    Zomwe tawerenga.

    (KOLASI)

    Chakudya chofunikira

    Ndi Mawu a M’lungu.

    Moyo umafunikadi

    Mawu a Mulungu.

(Onaninso Yos. 1:8; Aroma 15:4.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena