Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 144
  • Mukhulupirikebe

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mukhulupirikebe
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Yang’ananibe Pamphotho!
    Imbirani Yehova
  • Yang’ananibe Maso Anu Pamphotho!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Musalole Kuti Chilichonse Chikulepheretseni Kulandira Mphoto
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Tizilalikira Anthu a Mitundu Yonse
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 144

NYIMBO 144

Mukhulupirikebe

Losindikizidwa

(2 Akorinto 4:​18)

  1. 1. Pomwe osaona aona,

    Ovutika kumva akumva,

    Ana akuimbatu nyimbo,

    Mtendere padziko lonse.

    Pomwe akufa akuuka,

    Uchimo ndi mavuto zatha.

    (KOLASI)

    Mudzaona zinthu zonsezi,

    Mukakhulupirikabe.

  2. 2. Mimbulu ikudya ndi nkhosa,

    Mikango ikudya ndi ng’ombe,

    Mwana akuzitsogolera,

    Zikumvera mawu ake.

    Pomwe misozi yonse yatha,

    Mantha ndi zopweteka zatha.

    (KOLASI)

    Mudzaona zinthu zonsezi,

    Mukakhulupirikabe.

(Onaninso Yes. 11:​6-9; 35:​5-7; Yoh. 11:24.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena