15 Chihema Chopatulika Chimene Achifotokoza mu Ekisodo 26
(Onani m’Baibulo lenileni kuti mumvetse izi)
Malo Oyera Koposa
Malo Oyera
Mafelemu Ochirikiza M’makona
Mafelemu Oimika
Mpiringidzo
Nsalu Yotchinga
Mzati
Nsalu Zopangira Hema
Nsalu Ubweya wa Mbuzi
Zophimba
Zikopa za Nkhosa Zamphongo Zikopa za Akatumbu
Nsalu Yotchinga
Mzati
Zitsulo Zamkuwa Zokhazikapo Mizati
Tebulo la Mkate Wachionetsero
Choikapo Nyale
Guwa la Nsembe Zofukiza Zonunkhira
Zitsulo Zasiliva Zokhazikapo Mizati
Likasa
Zitsulo Zokhazikapo Mafelemu Oimika
Mphete za Mpiringidzo