Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • nwt tsamba 2220-2221
  • B5 Chihema Chopatulika Komanso Mkulu wa Ansembe

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • B5 Chihema Chopatulika Komanso Mkulu wa Ansembe
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Nkhani Yofanana
  • “Chilimikani ndi Kuona Chipulumutso cha Yehova”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
B5 Chihema Chopatulika Komanso Mkulu wa Ansembe

B5

Chihema Chopatulika Komanso Mkulu wa Ansembe

Losindikizidwa

Mbali za Chihema Chopatulika

  1. 1 Likasa (Eks. 25:10-22; 26:33)

  2. 2 Katani (Eks. 26:31-33)

  3. 3 Chipilala Chopachikapo Katani (Eks. 26:31, 32)

  4. 4 Malo Oyera (Eks. 26:33)

  5. 5 Malo Oyera Koposa (Eks. 26:33)

  6. 6 Nsalu Yotchinga Khomo la Chihema (Eks. 26:36)

  7. 7 Chipilala Chopachikapo Nsalu Yotchinga Khomo (Eks. 26:37)

  8. 8 Zitsulo Zakopa Zokhazikapo Zipilala (Eks. 26:37)

  9. 9 Guwa Lansembe Zofukiza (Eks. 30:1-6)

  10. 10 Tebulo la Mkate Wachionetsero (Eks. 25:23-30; 26:35)

  11. 11 Choikapo Nyale (Eks. 25:31-40; 26:35)

  12. 12 Nsalu ya Tenti (Eks. 26:1-6)

  13. 13 Nsalu ya Tenti ya Ubweya wa Mbuzi (Eks. 26:7-13)

  14. 14 Zikopa za Nkhosa Zophimbira (Eks. 26:14)

  15. 15 Zikopa za Akatumbu Zophimbira (Eks. 26:14)

  16. 16 Mafelemu Oimika (Eks. 26:15-18, 29)

  17. 17 Zitsulo Zasiliva Zokhazikapo Mafelemu Oimika (Eks. 26:19-21)

  18. 18 Ndodo (Eks. 26:26-29)

  19. 19 Zitsulo Zasiliva (Eks. 26:32)

  20. 20 Beseni Losambira Lakopa (Eks. 30:18-21)

  21. 21 Guwa Lansembe Zopsereza (Eks. 27:1-8)

  22. 22 Bwalo (Eks. 27:17, 18)

  23. 23 Khomo la Bwalo (Eks. 27:16)

  24. 24 Nsalu Zotchingira Mpanda (Eks. 27:9-15)

Mkulu wa Ansembe

Chaputala 28 cha buku la Ekisodo chimafotokoza mwatsatanetsatane zovala za mkulu wa ansembe wa Isiraeli

  • Nduwira (Eks. 28:39)

  • Chizindikiro Chopatulika cha Kudzipereka (Eks. 28:36; 29:6)

  • Mwala wa Onekisi (Eks. 28:9)

  • Tcheni (Eks. 28:14)

  • Chovala Pachifuwa Chachiweruzo Chokhala ndi Miyala 12 Yamtengo Wapatali (Eks. 28:15-21)

  • Efodi Ndiponso Lamba Wake Woluka (Eks. 28:6, 8)

  • Malaya Odula Manja Abuluu (Eks. 28:31)

  • Mpendero Wokhala ndi Mabelu ndi Makangaza (Eks. 28:33-35)

  • Mkanjo Wamandalasi Waulusi Wabwino (Eks. 28:39)

  • Tchati Chosonyeza Nthawi

  • 1512 B.C.E. Chihema chopatulika chinamalizidwa

  • 1026 B.C.E. Kachisi anatseguliridwa

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena