Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2016
“Zikomo kwambiri chifukwa magaziniwa ndi a panthawi yake.”—Amy
Amy ndi mayi yemwe amaona kuti nkhani za m’magazini a Galamukani! ndi zothandiza pa moyo wake watsiku ndi tsiku. Mofanana ndi mayiyu, palinso anthu mamiliyoni ambiri amene magaziniwa amawathandiza kwambiri. Pitani pawebusaiti ya www.jw.org/ny kuti muwerenge nkhani zimene zasonyezedwa m’munsimu.
ANTHU AKALE
CHIPEMBEDZO
Kodi Baibulo Langokhala Buku Labwino Basi? Na. 2
Kodi Baibulo Limalola Kuti Akazi Kapena Amuna Okhaokha Azigonana? Na. 4
Kodi Nkhani Yonena za Yesu Ndi Yongopeka? Na. 5
KUCHEZA NDI ANTHU
Katswiri Woona za Mmene Ana Osabadwa Amakulira Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake (Y. Hsuuw): Na. 2
KUCHITA ZINTHU NDI ANTHU
Kodi Mungasonyezane Bwanji Ulemu? (mwamuna ndi mkazi wake): Na. 6
Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi Anzanu Apamtima? Na. 1
Kuphunzitsa Mwana Wanu Nkhani Zokhudza Kugonana: Na. 5
Mungatani Kuti Musamakangane Pokambirana Mavuto Anu? (mwamuna ndi mkazi wake): Na. 3
Zimene Mungachite Mwana Akatsala Pang’ono Kutha Msinkhu: Na. 2
MAYIKO NDI ANTHU
MBONI ZA YEHOVA
A Mboni za Yehova Akumasulira M’zinenero Zambiri: Na. 3
Kodi Mumadziwa Zotani Zokhudza a Mboni za Yehova? Na. 1
“Mfundozi Zindithandiza Kwambiri” (jw.org): Na. 5
NYAMA NDI ZOMERA
SAYANSI
Chinthu Chodabwitsa (kaboni): Na. 5
Kanyama Kam’madzi Komwe Kamasinthasintha Mtundu: Na. 1
Khosi la Nyerere: Na. 3
Nyenje za Moyo Wautali: Na. 4
Ulusi wa Nkhono Yam’madzi: Na. 6
UMOYO NDI MANKHWALA
Kodi Kudana ndi Kusagwirizana ndi Zakudya kwa Thupi N’kosiyana Bwanji? Na. 3
Kodi Tingapewe Bwanji Matenda? Na. 6
ZIMENE BAIBULO LIMANENA
Chikhulupiliro: Na. 3
Kukongola: Na. 4
Kumwamba: Na. 1
Kusunga Nthawi: Na. 6
Kuyamikira: Na. 5
Nkhawa: Na. 2