BOKOSI 8A
Ulosi Wokhudza Mesiya—Mtengo Waukulu Wamkungudza
Losindikizidwa
EZEKIELI 17:3-24
1. Nebukadinezara anatenga Yehoyakini n’kupita naye ku Babulo
2. Nebukadinezara anasankha Zedekiya kukhala mfumu ku Yerusalemu
3. Zedekiya anapandukira Yehova ndipo anapita ku Iguputo kukapempha kuti amuthandize pa nkhondo
4. Yehova anaika Mwana wake pa Phiri la Ziyoni wakumwamba
5. Yesu akamadzalamulira monga mfumu, anthu omvera azidzakhala motetezeka