BOKOSI 10A
Kulambira Koyera—Kunabwezeretsedwa Pang’onopang’ono
Losindikizidwa
“Gobedegobede”
William Tyndale ndi anzake anamasulira Baibulo m’Chingelezi komanso m’zilankhulo zina
“Mitsempha ndi mnofu”
Charles T. Russell ndi anzake anabwezeretsa choonadi cha m’Baibulo
“Iwo anakhala ndi moyo ndipo anaimirira”
Anthu a Yehova ‘atakhala ndi moyo’ mu 1919, anayamba kugwira ntchito yolalikira mwakhama