BOKOSI 22A
Kukumana ndi Mayesero Omaliza
Losindikizidwa
Anthu Adzakhalanso Angwiro—1 AKOR. 15:26
Yesu Adzapereka Ufumu kwa Yehova—1 AKOR. 15:24
Satana Adzamasulidwa Kuchokera Kuphompho; Anthu Opanduka Adzakhala Kumbali ya Satana pa Kuukira Komaliza—CHIV. 20:3, 7, 8
Opanduka Onse Adzawonongedwa—CHIV. 20:9, 10, 15
Anthu Adzakhala ndi Moyo Wosatha, Mwamtendere Komanso Mogwirizana—AROMA 8:19-21