Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 8/11 tsamba 7
  • Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
km 8/11 tsamba 7

Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu

Mafunso otsatirawa tidzawakambirana pa Sukulu ya Utumiki wa Mulungu ya mlungu woyambira August 29, 2011.

1. Kodi kukoma mtima kwa Mulungu “n’kwabwino kuposa moyo” motani? (Sal. 63:3) [w01 10/15 tsa. 15 ndime 17]

2. Kodi Salimo 70 likutiuza chiyani za Davide? [w08 9/15 tsa. 4 ndime 4]

3. Kodi lemba la Salimo 75:5 likutichenjeza za chiyani? [w06 7/15 tsa. 11 ndime 2]

4. Kodi ndi nthawi iti makamaka pamene tingayembekezere Yehova kumva mapemphero athu? (Sal. 79:9) [w06 7/15 tsa. 12 ndime 5]

5. Kodi tingaphunzire chiyani pa lemba la Salimo 90:7, 8 pa nkhani ya ‘machimo obisika’? [w01 11/15 tsa. 12-13 ndime 14-16]

6. Kodi mawu a pa Salimo 92:12-15 amasonyeza kuti anthu achikulire ali ndi udindo wofunika wotani mumpingo? [w04 5/15 tsa. 13-14 ndime 15-18]

7. Polemba mawu a pa Salimo 102:25-27, kodi wamasalimo ankatsutsa cholinga cha Mulungu cha dziko lapansi? (Gen. 1:28) [w08 4/1 tsa. 12 ndime 1]

8. Kodi lemba la Salimo 106:7 likutiphunzitsa chiyani pa nkhani ya kufunika kokhala ozindikira? [w95 9/1 tsa. 19 ndime 4–tsa. 20 ndime 2]

9. Malinga ndi Salimo 110:1, 4, kodi Yehova anachita lumbiro lotani kwa mbewu yolonjezedwa, kapena kuti Mesiya, nanga zimenezi zidzathandiza bwanji kuti mtundu wonse wa anthu udalitsidwe? [cl tsa. 194 ndime 13]

10. Kodi kusinkhasinkha za ubwino wotumikira Mulungu kunamuthandiza bwanji wamasalimo? (Sal. 116:12, 14) [w09 7/15 tsa. 29 ndime 4-5]

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena