LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano

Za m’Buku la Yohane

YOHANE

ZA M’BUKULI

  • 1

    • Mawuyo anakhala munthu (1-18)

    • Umboni umene Yohane M’batizi anapeleka (19-28)

    • Yesu, Mwanawankhosa wa Mulungu (29-34)

    • Ophunzila oyamba a Yesu (35-42)

    • Filipo ndi Nataniyeli (43-51)

  • 2

    • Phwando la ukwati ku Kana; asandutsa madzi kukhala vinyo (1-12)

    • Yesu ayeletsa kacisi (13-22)

    • Yesu amadziwa za mumtima mwa anthu (23-25)

  • 3

    • Yesu ndi Nikodemo (1-21)

      • Kubadwanso (3-8)

      • Mulungu anakonda dziko (16)

    • Umboni wothela wa Yohane wonena za Yesu (22-30)

    • Wocokela kumwamba (31-36)

  • 4

    • Yesu ndi mayi wacisamariya (1-38)

      • Lambilani Mulungu “motsogoleledwa ndi mzimu komanso coonadi.” (23, 24)

    • Asamariya ambili akhulupilila Yesu (39-42)

    • Yesu acilitsa mwana wamwamuna wa munthu wina wotumikila mfumu (43-54)

  • 5

    • Munthu wodwala acilitsidwa ku Betesida (1-18)

    • Yesu apatsidwa mphamvu ndi Atate wake (19-24)

    • Akufa adzamva mawu a Yesu (25-30)

    • Maumboni okamba za Yesu (31-47)

  • 6

    • Yesu adyetsa anthu 5,000 (1-15)

    • Yesu ayenda pamadzi (16-21)

    • Yesu ndi “cakudya copatsa moyo” (22-59)

    • Ambili apunthwa ndi mawu a Yesu (60-71)

  • 7

    • Yesu ku Cikondwelelo ca Misasa ca Ayuda (1-13)

    • Yesu aphunzitsa ku cikondwelelo (14-24)

    • Anthu akhala ndi maganizo osiyanasiyana pa nkhani yokhudza Khristu (25-52)

  • 8

    • Atate acitila umboni za Yesu (12-30)

      • Yesu ndi “kuwala kwa dziko” (12)

    • Ana a Abulahamu (31-41)

      • ‘Coonadi cidzakumasulani’ (32)

    • Ana a Mdyelekezi (42-47)

    • Yesu ndi Abulahamu (48-59)

  • 9

    • Yesu acilitsa munthu amene anabadwa wakhungu (1-12)

    • Munthu wocilitsidwa afunsidwa mafunso ndi Afarisi (13-34)

    • Khungu la Afarisi (35-41)

  • 10

    • M’busa ndi makola a nkhosa (1-21)

      • Yesu ndi m’busa wabwino (11-15)

      • “Ndili ndi nkhosa zina” (16)

    • Ayuda akumana ndi Yesu ku Cikondwelelo ca Kupatulila Kacisi (22-39)

      • Ayuda ambili akana kukhulupilila (24-26)

      • “Nkhosa zanga, zimamvela mawu anga” (27)

      • Mwana ndi wogwilizana ndi Atate (30, 38)

    • Ambili akhulupilila ku tsidya lina la Yorodano (40-42)

  • 11

    • Imfa ya Lazaro (1-16)

    • Yesu atonthoza Marita ndi Mariya (17-37)

    • Yesu aukitsa Lazaro (38-44)

    • Akonza ciwembu cakuti aphe Yesu (45-57)

  • 12

    • Mariya athila mafuta pa mapazi a Yesu (1-11)

    • Yesu atamandidwa polowa mu Yerusalemu (12-19)

    • Yesu akambilatu za imfa yake (20-37)

    • Kusowa cikhulupililo kwa Ayuda kukwanilitsa ulosi (38-43)

    • Yesu anabwela kudzapulumutsa dziko (44-50)

  • 13

    • Yesu asambika mapazi a ophunzila ake (1-20)

    • Yesu azindikila kuti Yudasi ndiye adzamupeleka (21-30)

    • Lamulo latsopano (31-35)

      • “Ngati mumakondana wina ndi mnzake” (35)

    • Yesu akambilatu kuti Petulo adzamukana (36-38)

  • 14

    • Yesu ndiye njila yokhayo yofikila kwa Atate (1-14)

      • “Ine ndine njila, coonadi, ndi moyo” (6)

    • Yesu alonjeza mzimu woyela (15-31)

      • ‘Atate ndi wamkulu kuposa ine’ (28)

  • 15

    • Fanizo la mtengo wa mpesa weniweni (1-10)

    • Lamulo la kuonetsa cikondi ngati ca Khristu (11-17)

      • ‘Palibe munthu amene ali ndi cikondi cacikulu kuposa ici’ (13)

    • Dziko lidana ndi ophunzila a Yesu (18-27)

  • 16

    • Ophunzila a Yesu akhoza kuphedwa (1-4a)

    • Nchito ya mzimu woyela (4b-16)

    • Cisoni ca ophunzila cidzasanduka cimwemwe (17-24)

    • Yesu agonjetsa dziko (25-33)

  • 17

    • Pemphelo lothela la Yesu pamodzi ndi atumwi ake (1-26)

      • Anthu adzapeza moyo wosatha akamadziwa Mulungu (3)

      • Akhristu sali a dziko (14-16)

      • “Mawu anu ndiwo coonadi” (17)

      • “Ndawadziwitsa dzina lanu” (26)

  • 18

    • Yudasi apeleka Yesu (1-9)

    • Petulo agwilitsa nchito lupanga (10, 11)

    • Yesu apelekedwa kwa Anasi (12-14)

    • Petulo akana Yesu koyamba (15-18)

    • Yesu aonekela pamaso pa Anasi (19-24)

    • Petulo akana Yesu kaciwili komanso kacitatu (25-27)

    • Yesu aonekela pamaso pa Pilato (28-40)

      • “Ufumu wanga si wa m’dzikoli” (36)

  • 19

    • Yesu akwapulidwa ndi kunyodoledwa (1-7)

    • Pilato afunsanso Yesu mafunso (8-16a)

    • Yesu akhomeleledwa pamtengo ku Gologota (16b-24)

    • Yesu akonza zakuti amayi ake asamalidwe (25-27)

    • Imfa ya Yesu (28-37)

    • Yesu aikidwa m’manda (38-42)

  • 20

    • Manda opanda kanthu (1-10)

    • Yesu aonekela kwa Mariya Mmagadala (11-18)

    • Yesu aonekela kwa ophunzila ake (19-23)

    • Thomasi akayikila koma pambuyo pake akhulupilila (24-29)

    • Colinga ca mpukutu uwu (30, 31)

  • 21

    • Yesu aonekela kwa ophunzila ake  (1-14)

    • Petulo atsimikizila Yesu kuti amamukonda (15-19)

      • “Dyetsa ana anga a nkhosa” (17)

    • Tsogolo la ophunzila okondedwa a Yesu (20-23)

    • Mapeto ake (24, 25)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani